Docsity
Docsity

Prepare-se para as provas
Prepare-se para as provas

Estude fácil! Tem muito documento disponível na Docsity


Ganhe pontos para baixar
Ganhe pontos para baixar

Ganhe pontos ajudando outros esrudantes ou compre um plano Premium


Guias e Dicas
Guias e Dicas


Molecular atómica siple, Resumos de Química

Química analítica molecular atómica

Tipologia: Resumos

2026

Compartilhado em 21/06/2026

solomo-maquesson
solomo-maquesson 🇲🇿

2 documentos

1 / 2

Toggle sidebar

Esta página não é visível na pré-visualização

Não perca as partes importantes!

bg1
pf2

Pré-visualização parcial do texto

Baixe Molecular atómica siple e outras Resumos em PDF para Química, somente na Docsity!

? + y | É MN 60 Kodi Muli ndi Cholinga Chotani pa Moyo Wanu? — Na. | ' y : =, fl ene % tpandizant anthu amene sadziwa zambiri zokhudza Baibulo a arólinga f “OZ ANI as uti Ku Mulungu amene amawaganizira, kudziwa mmene angasan sakhulupl a ito Zi | kuti no pa moyo WaWo. Ngati mungakonde, mukhozanso kugwiritsa ntchito zithun abwi , : iotokozere míundo Za m'malo omwe asonyezedwa KODI MUNGASANKHE BWANJI ZOLINGA PA MOYO WANU? (4 min.) , munthu amakhala ndi cholinga potengera dera la kwawo kapena banja limene anakulira Ena amakhala ndi zolinga potengera mtundu wawo kapena udindo umene ali nawo ku panja kwawo ' Anthu ena amakhala ndi cholinga chochita ma kapena kukhala olemera ' Zomwe timakhulupirira zokhudza Mulungu zikhoza kusintha kwambiri cholinga chathu pa moyo (g 3/15 4 1-4) phunaziro a ku yunivesite, kukhala otchuka, Pali zinthu zimene timaona zomwe zimatitsimikizira kúti kuli Miengi, komabe anthu ambiri samudziwa (Aro 1:19, 20; Ahe 3:4) KODI MLENGIWATHU NDI NDANI? (6 min.) Ee Baibulo limaphunzitsa kuti Mulungu si mphamvu chabe, koma ndi Atate wathu wachikondi ' amene dzina lake ndi Yehova [Werengani Yesaya 42:8] (Mt 6:9; w20.02 3 4) Iye ali ndi makhalidwe ambiri abwino, ndipo khalidwe lake lalikulu ndi chikondi (Eks 34:6; 1Yo 4:8) : Yehova analenga zinthu zonse ndi cholinga kuphafikizapo ifeyo (Mia 12:13; Yes 45:18; w77 29 E E lye amatikonda kwambiri ndipo zimene timachita pa moyô wathu zimamukhudza (SI 32:8) de e TIKHOZA “KUY ANDIKIRA MULUNGU" (7 min.) Yehova akutipempha kuti tikhale anzake [Werengani Yakobo 4:8] [Chithunzi 1 Timamudziwa bwino tikamaphúnzira Baibulo (Yoh 17:3: w15 4/15 21 47) Tikhoza kulankhula naye momasuka mpemphero (S| 62:8. 65:2) Zinthu zimatiyendera pwino tikamayandikira Mulungu (S| 73:28; Ye M'Baibulo, timapezamo nzeru zothandiza zochokera kwa Mle [Fotokozani zimene zinachitikira ena zoSonyeza kuti moyo w atadziwa Yehova. Mwachitsanzo, onani Nsanja ya Olonda, 10-11, 13-14) s 48:17, 18) ngi wathu (wp17.1 6-7) awo unasintha kwambiri ya November 1, 2012, tsa em gama” Al CHOLINGA CHATHU CHIMASINTEA ria YEHOVA (8 min.) Munthu akadziwa Yehova ama à Eds o lngê ea ayendera a | kuti ndi zofunika kwambirt ngakhaie amba k Zake pa Moyo » Zinthu zimene amaziona | Tikamamudziwa bwino yehova, E É UMukonda k Tiyenera kumakonda kwambiri Ye YPosa anthu Wambiri (Mko 12 . 28-30) ; e ithandiza kuchita 2; Omwe t ps — * Kukonda kwambiri vyenova kumatit £inthu zo Satirazi “mafuna kuwasahgalatsa gs Na. 60 Kodi Muli ndi Cholinga Chotani pa Moyo Wanu? Tsamh Timatsatira malangizo a Mulungu omwe ndi achikondí (Miy 3:5, 6) Timakhala ofunitsitsa kusintha pa chilichonse kuti likhale anzake (SI 37:5) [Chithunzi2) Timasankha kuti tisamagwiritse ntchito dzikoli “mokwanira” (1Ak 7:31) Vimaona kuti kuthandiza ena kudziwa Yehova n'kofunika kwambiri (Mt 6:33) Timavomereza kuti tikhale anthu a Mulungu (Aro 14:8; 1Pe 3:21; w20.03 9 4-5) [Chithunzi 3] a ; Si Tikadzipereka kwa Mulúngu, timaona kuti cholinga chathu pa moyo di kuchita zimene Mulungu amafuna (1Pe 4:2) Timasamalira maudindo athu m'banja komanso maudindo ena mrnjira imene imalemekeza Mulungu MUKHOZA KUKHALA NDI CHOLINGA CHABWINO PA MOYO WANU (5 min.) Tonsefe tiyenera kusankha zimene timafuna kuchita pa moyo wathu Tikamangokhalira kufunafuna chuma timakumana ndi mavuto ambiri komanso timakhala OSasangalata (Miy 23:4, 5) - Sitingathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi' (Mt 6:19, 20, 24) Tikasankha kulambira Yehova timakhala ndi moyo wabwino komanso wosangalala [Werengani Miyambo 10:22] E | Pitirizani kuphunzi Mukamagwiritsa ntchito “(1Yo 2:17) E “TT satirani kwambiri autilainiyi, ndj wa pa dl Sikuti mukuyenera Ft a ai yosonyezan Ona * Utumiki, tsa, 52-55, 166169) otokoza matem Pd a ubwenzi wanu ndi iye . j imbits ra za Mulungu ndipo musasiye kulimbit kudalitsani mpaka kalekale Toyo wanu potamanda Yehova, iye adza ni buku la Sukulu ya Rd IKAMBIDWE 30 MINITSI 2021 Watch Tower Bible and Tra A á 2N Na. 60 9/21 A Society of Pennsylvania pinta it Souttl Afiica JNVSA z